April 27–May 3
GENESIS 34-35
Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa”: (10 min.)
Ge 34:1—Dina ankakonda kucheza ndi atsikana achikanani (w97 2/1 30 ¶4)
Ge 34:2—Sekemu anagwiririra Dina (lvs 124 ¶14)
Ge 34:7, 25—Simiyoni ndi Levi anapha Sekemu komanso amuna onse a mumzinda wake (w09 9/1 21 ¶1-2)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ge 35:8—Kodi Debora anali ndani, nanga tingaphunzire chiyani kwa iye? (it-1 600 ¶4)
Ge 35:22-26—Kodi tikudziwa bwanji kuti si nthawi zonse pamene mwana woyamba kubadwa ankayenera kukhala mumzere wa makolo a Mesiya? (w17.12 14)
Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 34:1-19 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi Elise anachita chiyani kuti amufike pamtima womvetsera wake? Kodi tingayambitse bwanji phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa?
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 13)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 4 ¶6-7 (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chotsani Milungu Yachilendo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Tsutsani Mdyerekezi”.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 82
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitilira 3 min.)
Nyimbo Na. 83 ndi Pemphero