February 20-26
YESAYA 58-62
Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tikalengeze za Chaka cha Yehova Chokomera Anthu Mtima”: (10 min.)
Yes. 61:1, 2
—Yesu anadzozedwa kuti ‘alengeze chaka cha Yehova chokomera anthu mtima’ (ip-2 322 ¶4) Yes. 61:3, 4
—Yehova amatipatsa “mitengo ikuluikulu ya chilungamo” kuti izitithandiza pa ntchito yake (ip-2 326-327 ¶13-15) Yes. 61:5, 6
—“Anthu ochokera kwina” amagwirizana ndi “ansembe a Yehova” pogwira ntchito yaikulu yolalikira padziko lonse (w12 12/15 25 ¶5-6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yes. 60:17
—Kodi Yehova wakwaniritsa bwanji lonjezoli m’masiku otsiriza ano? (w15 7/15 9-10 ¶14-17) Yes. 61:8, 9
—Kodi “pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale” n’chiyani, nanga “ana” ndi ndani? (w07 1/15 11 ¶6) Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 62:1-12
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.1 chikuto
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.1 chikuto
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 15 ¶19
—Ngati n’zotheka, chitsanzochi chikhale cha mayi akuphunzira ndi mwana wake wamkazi.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 47
Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo mu Utumiki: (6 min.) Nkhani. Onetsani vidiyo yakuti Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Limbikitsani abale ndi alongo kugwiritsa ntchito vidiyoyi mu March ndi April pokambirana ndi anthu pa ulendo woyamba kapena wobwereza.
“Tizigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mabuku Ndiponso Magazini”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Ntchito Yotumiza Mabuku ku Congo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 18 ¶1-13
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero