July 31–August 6
NEHEMIYA 3-4
Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ne 4:17, 18—Kodi munthu angagwire bwanji ntchito yomanga ndi dzanja limodzi? (w06 2/1 9 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Ne 3:15-24 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Kambiranani tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo m’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)
Nkhani: (5 min.) km 11/12 1—Mutu: Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama. (th phunziro 10)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera kuti, Mogwirizana ndi zomwe mwaona muvidiyoyi, kodi khalidwe lathu pa malo ogwirira ntchito lingathandize bwanji anthu kukhala ndi maganizo oyenera okhudza a Mboni?
Zofunika Pampingo: (7 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 52
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero