June 11-17
Luka 1
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Luka.]
Luka 1:38—Mariya anavomera modzichepetsa kugwira ntchito imene Mulungu anamupatsa (ia 149 ¶12)
Luka 1:46-55—Iye anatamanda Yehova pofotokoza mfundo zochokera m’Mawu a Mulungu (ia 151 ¶15-16)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Luka 1:69—Kodi mawu akuti “nyanga yachipulumutso” amatanthauza chiyani? (“nyanga yachipulumutso” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 1:69, nwtsty)
Luka 1:76—Kodi Yohane M’batizi ‘anatsogola pamaso pa Yehova’ m’njira yotani? (“anatsogola pamaso pa Yehova” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 1:76, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 1:46-66
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zokhudza lemba la chaka cha 2018. (w18.01 8-9 ¶4-7)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 20 ¶1-6 komanso tsamba 211, 214-215
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero