Muzitsatira Malamulo Awiri Aakulu Kwambiri
Pogwiritsa ntchito lemba la Mateyu 22:36-39, lembani manambala kuyambira ndi chifukwa chachikulu chimene timapitira kumisonkhano yathu:
-
Kuti tikalimbikitsidwe
-
Kuti tikalimbikitse ena
-
Kuti tikalambire komanso kusonyeza kuti timakonda Yehova
N’chifukwa chiyani tiyenera kuyesetsa kupitabe kumisonkhano ngakhale titatopa kwambiri moti tikuona kuti sitingakapindule mokwanira?
Kodi ndi njira zina ziti zimene tingasonyezere kuti timamvera malamulo awiri aakulu kwambiri?