March 1-7
NUMERI 7–8
Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Nu 8:17—Kodi Yehova ankawaona bwanji ana aamuna oyamba kubadwa a mu Isiraeli? (it-1 835)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 7:1-17 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso munthu amene munkaphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso wachibale amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 17)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 123 ndi bokosi lakuti “Thukuta la Yesu Linaoneka Ngati Madontho a Magazi.”
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero