March 21-27
1 SAMUELI 16-17
Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 16:14, mawu a m’munsi—Kodi Sauli analandira “mzimu woipa wochokera kwa Yehova” m’njira yotani? (it-2 871-872)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 16:1-13 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. (th phunziro 11)
Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Itanirani mnzanu wakuntchito, wakusukulu kapena wachibale wanu amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Mudziwitseni za webusaiti yathu. (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Njira Zitatu Zimene Zingatithandize Kuti Tizidalira Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Palibe Chifukwa Choti Tiziopa Kuzunzidwa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 13 ndime 23-26, mfundo za m’Baibulo tsa. 184-186
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero