March 28–April 3
1 SAMUELI 18-19
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 19:23, 24—Kodi Mfumu Sauli anachita bwanji zinthu “ngati mneneri”? (it-2 695-696)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 18:25–19:7 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
“Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asiye Makhalidwe Oipa”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Asiye Makhalidwe Oipa.
Nkhani: (5 min.) km 1/03 1—Mutu: Ntchito Imene Imafunika Kudzichepetsa. (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 14 ndime 1-9
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero