March 7-13
1 SAMUELI 12-13
Nyimbo Na. 4 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kudzikuza Kumabweretsa Manyazi”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Sa 12:21—Kodi anthu ankatsatira bwanji zinthu ‘zopanda pake’? (w11 7/15 13 ¶15)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 12:1-11 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu—Mt 16:16. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 mawu oyamba komanso mfundo 1-2 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 13 ndime 1-12
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero