December 13-19
OWERUZA 8-9
Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 8:27—Kodi Gidiyoni ankalambira efodi yemwe anapanga? (it-1 753 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 8:28–9:6 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo. (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 mfundo 4 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 9 ndime 1-8, mawu akumapeto 23, 24
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero