CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yefita Anali Munthu Wauzimu
Yefita sanasungire ena zifukwa (Owe 11:5-9; w16.04 7 ¶9)
Yefita ankaphunzira zimene Yehova ankachita ndi anthu ake (Owe 11:12-15; it-2 27 ¶2)
Yefita ankaganizira nkhani yofunika kwambiri yakuti Yehova ndiye Mulungu woona (Owe 11:23, 24, 27; it-2 27 ¶3)
Kodi ndi zinthu ziti zimene ndimachita zomwe zimasonyeza kuti ndine munthu wauzimu?