CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Yochititsa Chidwi
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Oweruza.]
Yehova anapereka Ehudi kwa Aisiraeli kuti awapulumutse m’manja mwa Amowabu (Owe 3:15; w04 3/15 31 ¶3)
Ehudi anapha Egiloni ndipo anatsogolera Aisiraeli kuti apambane (Owe 3:16-23, 30; w04 3/15 30 ¶1-3)
Kodi nkhaniyi ikutiphunzitsa chiyani pa nkhani ya kulimba mtima komanso kudalira Yehova?