November 29–December 5, 2021
OWERUZA 4-5
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 5:20—Kodi nyenyezi zinamenya nkhondo motani kuchokera kumwamba pothandiza Baraki? (w05 1/15 25 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 4:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni Nsanja ya Olonda Na. 2 2021. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)
Nkhani: (5 min.) w06 3/1 28-29—Mutu: Kodi ‘akazi ayenera kukhala chete m’mipingo’ m’njira iti?—1Ak 14:34. (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Alongo Angatani Kuti Azichita Zambiri Potumikira Yehova?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Akazi Ogwira Ntchito Mwakhama Potumikira Ambuye”.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 8 ndime 8-18, mawu akumapeto 22
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero