November 8-14
YOSWA 20-22
Nyimbo Na. 120 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingaphunzire pa Kusamvana kwa Mafuko a Aisiraeli”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 21:43, 44—Kodi tinganene bwanji kuti mawuwa anali oona ngakhale kuti Akanani ambiri sanagonjetsedwe komanso sanalole kuti Aisiraeli aziwalamulira? (it-1 402 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 20:1–21:3 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Baibulo—Chv 21:3, 4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Ndipo kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 7 ndime 10-19, mawu akumapeto 21
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero