CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena
Elifazi anauza Yobu kuti anthu sangasangalatse Mulungu (Yob 15:14-16; w05 9/15 26 ¶4-5)
Elifazi anasonyeza kuti Yobu anali woipa ndipo n’chifukwa chake ankakumana ndi mavuto (Yob 15:20)
Mawu amene Elifazi analankhula sanatonthoze Yobu (Yob 16:1, 2)
Zomwe Elifazi anauza Yobu zinali zabodza. Yehova amatiyamikira kwambiri chifukwa cha khama lomwe timasonyeza pomutumikira. (Sl 149:4) Ngakhale anthu olungama amadziwa kuti azikumana ndi mavuto.—Sl 34:19.
FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndingatani kuti ‘ndizilankhula molimbikitsa kwa amtima wachisoni’?—1At 5:14; w15 2/15 9 ¶16.