Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
1. N’chifukwa chiyani ‘sitichita manyazi ndi uthenga wabwino’? (Aroma 1:16; 11:13)
2. Kodi timasonyeza bwanji kuti tili kumbali ya choonadi? (Mat. 10:32; Aroma 10:9)
3. Kodi n’chiyani chimatithandiza kuti tizilalikira bwino tikakhala mu utumiki? (2 Tim. 2:15)
4. Kodi tingatsanzire bwanji Onesiforo? (2 Tim. 1:7, 8)
5. Kodi timasonyeza bwanji kuti sitichita manyazi kukhala kumbali ya Mulungu wathu? (Aheb. 10:39; 1 Pet. 3:15; Yoh. 18:36; 1 Ates. 5:12, 13)
6. Kodi ‘timadzitama bwanji mwa Yehova’? (Sal. 34:1, 2; 1 Akor. 1:31)
© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-brpgm25-CN