Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2024-2025 Wokhala ndi Woyang’anira Dera
“Makhalidwe Anu Akhale Ogwirizana ndi Uthenga Wabwino”
Pulogalamu ya chigawo cha m’mawa ndi masana cha msonkhano wadera wokhala ndi woyang’anira dera.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunso amenewa adzayankhidwa pamsonkhanowu.