Mfundo Zanga—Kugonana, Makhalidwe ndi Chikondi
Gawo 4
Mfundo Zanga—Kugonana, Makhalidwe ndi Chikondi
Lembani mfundo zitatu zimene mukufuna kuti muzizitsatira. Pa mfundo iliyonse mulembenso chifukwa chake mukuona kuti ndi nzeru kutsatira mfundoyo. *
1. ․․․․․
2. ․․․․․
3. ․․․․․
[Mawu a M’munsi]
^ ndime 3 Mwachitsanzo, “Ndiziyesetsa kupewa kugonana ndi munthu mpaka ndidzalowe m’banja ndipo ndikukhulupirira kuti kuchita zimenezi ndi nzeru chifukwa . . .” Onetsetsani kuti mwalemba zimene inuyo mwasankha kuchita osati kungotengera wina.