Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse

Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse

PADZIKO LONSE

  • MAYIKO 239

  • OFALITSA 8,201,545

  • MAOLA ONSE AMENE TINATHERA MU UTUMIKI WAKUMUNDA 1,945,487,604

  • MAPHUNZIRO A BAIBULO 9,499,933

M'CHIGAWO ICHI

Africa

Werengani zimene Mboni za Yehova zachita pophunzitsa anthu ku Angola, Congo (Kinshasa), Ghana, Nigeria, ndi South Africa mu 2014.

North ndi South America

Werengani ntchito yathu yophunzitsa Baibulo ku Argentina, Brazil, Haiti, Paraguay, ndi ku Suriname mu 2014.

Ku Asia ndi ku Middle East

Werengani ntchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu ku Indonesia, Mongolia, ku Philippines, ndi ku dziko lina la ku Asia mu 2014.

Europe

Werengani ntchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu ku Bulgaria, Finland, Germany, Romania, Russia, Spain ndi ku Sweden mu 2014.

Oceania

Werengani ntchito yathu yophunzitsa anthu ku Kiribati, Marshall Islands, Papua New Guinea ndi ku Vanuatu mu 2014.