Pulogalamu ya 2018-2019 ya Msonkhano Wadera wa Mboni za Yehova Wokhala ndi Woimira Nthambi
Onani pulogalamu ya msonkhano waderawu yosonyeza nkhani zimene mlendo woimira nthambi adzakambe.
Muzichita Zinthu Mwamphamvu
Msonkhanowu ufotokoza zimene tingachite kuti tipeze mphamvu yotithandiza kukhala olimba m’chikhulupiriro.
Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunsowa adzayankhidwa pa msonkhanowu.