Khalani Olimba Mtima
M’MAWA
-
9:30 Kumvetsera Nyimbo
-
9:40 Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero
-
9:50 Yehova Amatithandiza Kukhala Olimba Mtima
-
10:05 Nkhani Yosiyirana: Khalani Olimba Mtima Ngati . . .
-
Inoki
-
Mose
-
Yehosafati
-
Petulo
-
-
11:05 Nyimbo Na. 69 ndi Zilengezo
-
11:15 Muzilimba Mtima mu Utumiki
-
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
-
12:00 Nyimbo Na. 48
MASANA
-
1:10 Kumvetsera Nyimbo
-
1:20 Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero
-
1:30 Nkhani ya Onse: Muzisonyeza Kuti Muli Kumbali ya Kulambira Koona
-
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
-
2:30 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
-
2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzilimba Mtima Ngati Yesu Mukamakumana ndi Mavuto
-
M’banja
-
Kusukulu
-
Kuntchito
-
Kumene Mumakhala
-
-
3:40 Anthu Olimba Mtima Adzalandira “Mphoto Yaikulu Kwambiri”
-
4:15 Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero