Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
N’chifukwa chiyani sitiyenera kukayikira kuti Yehova atilimbitsa mtima tikamupempha? (Sal. 138:3)
Kodi tingatani kuti tikhale olimba mtima ngati atumiki a Mulungu akale? (Mac. 4:31)
Kodi tingalimbe bwanji mtima mu utumiki? (1 Ates. 2:2)
N’chiyani chimatithandiza kukhala olimba mtima tikamakumana ndi mavuto? (1 Pet. 2:21-23)
Kodi Akhristu olimba mtima adzalandira mphoto iti? (Aheb. 10:35)