“Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita”
M’MAWA
-
9:40 Kumvetsera Nyimbo
-
9:50 Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero
-
10:00 “Kondwerani Chifukwa cha Zimene Yehova Wachita Ndipo Sangalalani”
-
10:15 “Okonda Dzina Lanu Adzakondwa Chifukwa cha Inu”
-
10:30 ‘Muzidzazidwa ndi Chimwemwe’ pa Utumiki Wanu
-
10:55 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
-
11:05 Musalole Kuti Mitima Yanu ‘Ilemedwe’
-
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
-
12:05 Nyimbo Na. 51
MASANA
-
1:20 Kumvetsera Nyimbo
-
1:30 Nyimbo Na. 111
-
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
-
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
-
2:15 Nkhani Yosiyirana: Yehova Ndi Amene Amatithandiza Kuti Tizikhala Osangalala
-
• Tikamathandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira
-
• Tikamathandiza Okhulupirira Anzathu
-
• Tikamapirira Mayesero
-
-
3:00 Nyimbo Na. 2 ndi Zilengezo
-
3:10 Muziika Yehova Patsogolo Panu Nthawi Zonse
-
3:55 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero