Zisonyezero za Voliyumu 82 ya Galamukani!
Zisonyezero za Voliyumu 82 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Agogo, 5/8, 6/8
Anthu Amtima Wapachala, 12/8
Kodi Ndingam’kane Bwanji? 4/8
Kodi Ndingatani Kuti Kuŵerenga Baibulo Kuzindisangalatsa?, 9/8
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamade Nkhaŵa Kwambiri? 10/8
Kodi Tsopano Ndikhala Bwanji Pamene Abambo Atichokera?, 1/8
Kubwezera, 11/8
Kukhala N’chibwenzi, 2/8,
Kuzemba Panyumba, 3/8
Mapemphero, 7/8, 8/8
CHIPEMBEDZO
Dzina la Mulungu Linabutsa Mkangano, 12/8
Kodi Baibulo Ndi Mbiri Yodalirika? 3/8
Kuukira kwa Soviet, 5/8
CHUMA NDI NTCHITO
Inshuwalansi, 3/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Fêng Shui, 12/8
Kodi Akristu Ayenera Kupita ku Tchalitchi?, 3/8
Kodi Kulira Maliro N’kulakwa? 7/8
Kodi Maloto Ndi Mauthenga Ochokera kwa Mulungu? 4/8
Kodi Mulungu Ankakondwera ndi Malonda a Ukapolo? 9/8
Kodi Mulungu N’ngolekerera Motani? 10/8
Kodi Ndi Bwino Kuti Mulungu Azigwiritsa Ntchito Mphamvu? 11/8
Kodi Ukwati ndi Mgwirizano wa Moyo Wonse? 2/8
Kodi Yehova Anali Mulungu wa Fuko la Ayuda? 5/8
Kodi Zipembedzo Zonse ndi Misewu Yopita kwa Mulungu? 6/8
Kusankha Chithandizo cha Mankhwala, 1/8
Wokana Kristu, 8/8
MAUNANSI A ANTHU
Anthu Okalamba, 9/8
Kulangiza Ana, 11/8
Kupulumutsa Ukwati, 1/8
Kuthandiza Akazi Omenyedwa ndi Amuna, 11/8
Kuŵerengera Ana Mokweza Mawu, 12/8
Udani Wasanduka Mliri, 8/8
MAYIKO NDI ANTHU
Amene Anaukiridwa Kwambiri ndi Soviet, 5/8
Dera la Maluŵa Okongola Koposa (South Africa), 7/8
Kente—Nsalu ya Mafumu (Africa), 10/8
Kusintha Dera Louma Kukhala Lachonde (India), 4/8
Matatu—Galimoto za ku Kenya Zonyamula Apaulendo, 11/8
Mzinda wa mu Africa Umene uli ndi Anthu a Chikhalidwe Chosiyanasiyana (South Africa), 10/8
Ulendo Wokaona Malo ku Ghana, 6/8
Zoumba Zosunthasuntha za ku Namibia, 3/8
MBONI ZA YEHOVA
Anthu Ongodzipereka, 8/8
Kusefukira kwa Madzi ku Mozambique, 5/8
Maphunziro Othandiza kwa Moyo Wonse, 1/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Kulimbikitsa Mtendere M’malo mwa Nkhondo (D. Horle), 4/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Achinyamata Amene Akuvutika Maganizo, 9/8
Kulimbikitsa Odwala, 2/8
Mankhwala, 11/8
Matenda Opatsirana, 8/8
Moyo N’ngokoma (kudzipha), 11/8
Nyamakazi, 12/8
Thanzi Labwino kwa Onse, 6/8
Vuto Lokhala Wamantha Mukamakumbukira Zoopsa, 9/8
Ziŵerengero Zochititsa Mantha za AIDS, 3/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Dera la Maluŵa Okongola Koposa (South Africa), 7/8
Marabou—Mbalame Imene Amailakwira, 8/8
Nkhuku, 10/8
Zamoyo Zimadalirana, 12/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
‘Adzasula Malupanga Awo Kukhala Zolimira’—Liti? 3/8
Anthu Othandiza, 8/8
Kodi Padzikoli Madzi Akutha? 7/8
Kodi Tingadzale Chakudya Chokwanira? 10/8
Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Osokoneza Bongo, 7/8
Kupirira M’dziko Lotangwanitsa, 2/8
Mizinda Ili M’mavuto, 4/8
Ndende Zili Pamavuto, 5/8
Uchigaŵenga, 6/8
Udani Wasanduka Mliri, 8/8
Zida Zazing’ono, 4/8
ZOSIYANASIYANA
Kodi Kupulula Anthu Kungadzachitikenso? 6/8
Tsitsi, 4/8
Zakale Zingatiphunzitsenji, 3/8
Zikondwerero Zotchuka (Halloween), 10/8