Mlozera Nkhani wa Voliyumu 85 ya Galamukani!
Mlozera Nkhani wa Voliyumu 85 ya Galamukani!
ACHINYAMATA AKUFUNSA
Kugonana kwa pa Telefoni, 3/8
Kugonana Ndisanalowe M’banja, 8/8, 9/8
Kumwa Mowa Wambiri Nthawi Imodzi Kuli ndi Vuto Lanji? 10/8
Kupeza Nthawi Yochita Homuweki, 2/8
Malo Ovinira, 5/8
N’chifukwa Chiyani Chibwenzi Changa Chimandizunza Chonchi? 6/8
N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Tizivutika? 4/8
Ndingamuuze Bwanji Kuti Ndikumufuna? 11/8
Ndingatani Kuti Chibwenzi Changa Chisiye Kundizunza? 7/8
Ndingathe Bwanji Kukamba Nkhani Bwino Pagulu? 1/8
Ndingachite Chiyani Ndikalephera? 12/8
CHIPEMBEDZO
Kudziwa Dzina la Mulungu, 2/8
Mose Anali Munthu Weniweni Kapena Wongopeka? 4/8
CHUMA NDI NTCHITO
Kuvutitsidwa kuntchito, 5/8
MAUNANSI A ANTHU
Achinyamata Akamakula, 7/8
Atate Abwino, 9/8
Kulimbikitsa Ana Kuti Azikonda Kuphunzira, 8/8
Kusungulumwa, 6/8
Kupeza Anzanu Enieni, 12/8
Kuwerengera Ana, 11/8
Sukulu Yamkaka Yopanda Zoseweretsa, 10/8
Sungani Nthawi! 4/8
Zaka Zoyambirira za Moyo wa Mwana, 11/8
Zimene Ana Amafunikira Kwa Makolo, 1/8
MAYIKO NDI ANTHU
Anapulumuka Madzi Atasefukira! (Switzerland), 4/8
Mathithi (Zambia), 3/8
Msika wa Nsomba Waukulu Kwambiri Padziko Lonse (Japan), 2/8
Namaqualand (South Africa), 2/8
MBONI ZA YEHOVA
Achinyamata Amene Sachita Manyazi Kulankhula, 9/8
“Aliyense Ayenera Kuwerenga Buku Limeneli” (Mphunzitsi), 12/8
Banja Liyesedwa Chikhulupiriro, 5/8
Chikhulupiriro Chiyesedwa (Richmond Sixteen), 3/8
Khoti la ku Ulaya Linalemekeza Ufulu wa Mayi (France), 12/8
Msamariya Wachifundo Wamakono, 8/8
Zosuta Fodya Ine Ayi! (ndakatulo ya mtsikana), 5/8
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Chinthu Chabwino Kuposa Kutchuka (C. Sinutko), 9/8
Ndinaphunzitsidwa Kukonda Mulungu Kuyambira Ndili Mwana (A. Melnik), 11/8
“Yehova, Mwandipeza!” (N. Lenz), 10/8
SAYANSI
Kuyeza Dziko Lapansi ndi Ndodo, 7/8
Sayansi Ingakuthandizeni Kudziwa Mulungu? 7/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Banja Liyesedwa Chikhulupiriro (matenda a zilonda za m’mimba), 5/8
Chimfine Chobwera Mukakhala Pafupi ndi Mungu, 6/8
Kodi Edzi Idzatha Liti? 12/8
Kugona Tulo Tosakwanira, 2/8
Kunenepa Kwambiri, 11/8
Kusabereka, 10/8
Mankhwala Ochokera ku Zitsamba, 1/8
Matenda a Maganizo 1/8
Matenda a Misala, 12/8
Matenda Osintha Mtundu wa Khungu 10/8
Ngati Mwana Wakhanda Sasiya Kulira, 5/8
Nkhawa ya Maonekedwe Ikasanduka Matenda, 8/8
Nkhondo Yolimbana ndi Matenda, 6/8
Timafuniranji Chiyembekezo? 5/8
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Anthu Okalamba Tiyenera Kuwachitira Zinthu Motani? 10/8
Khalidwe Limayendera Gulu la Magazi? 2/8
Kodi Kusudzulana N’kuthetsadi Mavuto? 12/8
Kuda Nkhawa N’kupanda Chikhulupiriro? 6/8
Kulera Ana M’maleredwe a Mulungu, 11/8
Kumwa Mowa Mwauchidakwa N’koipadi? 3/8
Mulungu Amawaganiziradi Ana? 8/8
Mutu wa Banja, 7/8
N’chifukwa Chiyani Ukwati Tiyenera Kuuona Kuti N’ngopatulika? 5/8
N’zotheka Kusiya Zizolowezi Zoipa? 4/8
Zokambirana za Mayiko Zidzabweretsa Mtendere Padziko Lonse? 1/8
N’zotheka Kusiya Zizolowezi Zoipa? 4/8
Zokambirana za Mayiko Zidzabweretsa Mtendere Padziko Lonse? 1/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Chomera Chopirira Modabwitsa (welwitschia), 3/8
Lavenda, 7/8
Mphaka Amene Ali Pangozi Kwambiri (lynx wa ku Spain), 8/1
Ziweto, 3/8
Zomera N’zothandiza Popanga Mankhwala, 1/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Kudziteteza ku Anthu Oba Mwachinyengo, 8/8
Kusintha Zinthu, 4/8
Kutenga Mimba Ali Ana, 10/8
Nkhondo ya Nyukiliya Akuiopabe? 3/8
Tsankho, 9/8
ZOSIYANASIYANA
Chiwerengero cha Anthu, M’Baibulo, ndi M’tsogolo, 5/8
Chiyembekezo, 5/8
Kukhalabe Osangalala Ngakhale M’mavuto, 1/8
Kukonda Kuphunzira, 8/8
Matayala, 6/8
Mowa, 7/8
Zoseweretsa Ana Zabwino Kwambiri, 8/8