Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006
Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006
BAIBULO
Baibulo la M’chinenero Chamakono
CHIPEMBEDZO
Halowini, 10/06
Kodi Angelezi Oyambirira Kusamukira ku America Anali Akristu Oona? 2/06
Kodi Yesu Anali Ndani? 12/06
Kuyankha Funso Lovuta Kwambiri Loti “Chifukwa Chiyani?” 11/06
Michael Agricola (womasulira Baibulo), 1/06
Michael Servetus Anafufuza Choonadi Yekhayekha, 5/06
Mulungu Anagwiritsa Ntchito Chisinthiko? 9/06
MAUNANSI A ANTHU
Ana Ofunika Kuwasamalira Mwapadera, 4/06
Chikondi, 3/06
Kuthandiza Mwana Wanu Wamkazi Kukonzekera Kutha Msinkhu, 5/06
Mmene Mungakhalire ndi Banja Losangalala, 7/06
“Nthawi ya Chakudya Imatithandiza Kukondana,” 11/06
MAYIKO NDI ANTHU
Alhambra (ku Spain), 2/06
Aromani (Majipise), 10/06
Calypso—Nyimbo Zamakolo za ku Trinidad, 12/06
Chernobyl (ku Ukraine), 4/06
Chigwa Chotchedwa Death Valley (ku California), 11/06
Chilumba Chokongola Kwambiri cha Mchenga (Chilumba cha Fraser), 3/06
Mekong (mtsinje, wa ku Asia), 11/06
Michael Agricola “Anasintha Zinthu Kwambiri” (ku Finland), 1/06
Mlatho wa Tower Bridge Ndi Njira Yolowera mu London, 10/06
Mtsinje wa Thames (ku England), 2/06
Munda Wokongola Mogometsa (Gaudeloupe, ku Martinique), 5/06
Ulendo Wokaona Nkhosa Zam’tchire (ku Cyprus), 3/06
“Unabadwa kwa Makolo Oyera Kuposa Onse” (kupanga mchere, ku Brazil), 12/06
Uthenga Uyenera Kuperekedwa (kwa a Inca), 7/06
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Anakonda Zimene Anaphunzira, 12/06
Chikhulupiriro Chandithandiza Kupirira Matenda Oopsa (J. Stuart), 1/06
‘Ndidzadumpha Ngati Nswala’ (F. Abbatemarco), 8/06
‘Ndikufuna Kutumikira Mulungu Ndisanafe’ (M. Free), 3/06
Ndinali Mwana Wolowerera (M. W. Sunday), 12/06
Ndinali Wotaya Mtima Koma Tsopano Ndine Wosangalala (V. González), 7/06
Ndinaphunzira Kudalira Mulungu (E. Toom), 4/06
Ndinapulumutsidwa ku Masautso (J. François), 11/06
MBONI ZA YEHOVA
“Anaikidwa M’ndende Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo” (ku Auschwitz), 4/06
Chikhulupiriro cha Mwana (wodwala khansa), 8/06
Kumvera Machenjezo (Mphepo Yamkuntho ya Katrina), 6/06
Kuthandiza Mtsikana Wovutika Maganizo, 10/06
Kwa Owerenga (Galamukani!), 1/06
Misonkhano Yachigawo Yakuti “Chipulumutso Chayandikira,” 6/06
Mphatso ya Mtengo Wapatali (Buku la Mphunzitsi Waluso), 12/06
“Mumakondwerera Tsiku la Agogo Aakazi?” 12/06
“N’kabwino Kwabasi!” (kabuku ka ‘Onani Dziko Lokoma’), 2/06
“N’labwino Kwambiri” (Buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani), 11/06
SAYANSI
Chifukwa Chimene Timakhulupirira Kuti Kuli Mlengi, 9/06
‘Katswiri wa ku Britain Yemwe Anaiwalika’ (Robert Hooke), 7/06
Kodi Chisinthiko Chinachitikadi? 9/06
Kodi Mlengi Alipo? 9/06
Kukambirana ndi Katswiri wa Sayansi, 9/06
Maselo Ofiira a M’magazi, 1/06
Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wautali Bwanji? 5/06
N’chifukwa Chiyani Madzi a M’nyanja Zikuluzikulu Amakhala Amchere? 7/06
UMOYO NDI MANKHWALA
Kodi Kusisita Mwana N’kofunika? 7/06
Kulandira Mafoni Angozi—ku London, 3/06
Kupirira Matenda Oopsa, 1/06
Malo Opangira Ziwalo, 2/06
N’chifukwa Chiyani Magazi Ali Ofunika Kwambiri? 8/06
Nkhungu Imathandiza Komanso Imawononga 1/06
Nsomba Zikakudwalitsani, 7/06
Ukalamba, 2/06
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kucheza ndi Anzanga a ku Sukulu, 4/06
Muli Ndi Matenda Ovutika Kudya? 10/06
N’chifukwa Chiyani Amandiikira Malamulo Ambirimbiri? 12/06
N’chifukwa Chiyani Ndimadzivulaza? 1/06
Ndidzagwire Ntchito Yotani Pamoyo Wanga? 7/06
Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira Zokhudza Chilengedwe? 9/06
Ndingapewe Bwanji Zogonana Kusukulu? 3/06
Ndingatani Kuti Ndisiye Kudzivulaza? 2/06
Ndingatani Kuti Ndizisamala Ndalama? 6/06
Ndingathandize Bwanji Anthu Amene Akufunika Thandizo? 8/06
Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi? (kudziseweretsa maliseche), 11/06
Ndiziwerenga Chifukwa Chiyani? 5/06
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Anthu Akafa Amasanduka Angelo? 8/06
Kodi Mungathe Kuthandiza Anthu Akufa? 10/06
Kukhala Munthu Wamtendere N’kothandiza? 5/06
Kumwa Mowa, 12/06
Mzimu Woyera Ndi Munthu? 7/06
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kudalira Baibulo Kuti Lizititsogolera? 1/06
Ngati Anthu Akukondana Ndiye Kuti Palibe Cholakwika Atagonana Asanakwatirane? 11/06
Pali Mulungu Mmodzi Yekha Woona? 2/06
Sayansi Imatsutsana ndi Nkhani ya mu Genesis? 9/06
Tchimo Loyambirira Linali Chiyani? 6/06
Yesu Anaferadi Pamtanda? 4/06
Yesu Analidi Mwana wa Mulungu? 3/06
ZINYAMA NDI ZOMERA
Abulu, 12/06
Basi Adutsa! (atsekwe), 1/06
Dongosolo Lodabwitsa la Zomera, 9/06
Masiponji, 5/06
Mbalame za M’mphepete mwa Nyanja, 8/06
Nkhosa Zam’tchire, 3/06
Nthanga Imene Inazungulira Dziko (khofi), 3/06
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Uchigawenga, 6/06
ZOSIYANASIYANA
Bwato la ku Galileya, 8/06
Chimwemwe, 4/06
Kodi M’tsogolo Muli Zotani? 1/06
Kuba Magalimoto, 10/06
Kujambula Zithunzi, 6/06
Silika, 6/06
TV, 10/06
Zimene Mumakhulupirira Zili ndi Ntchito? 9/06