Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2007
Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2007
CHIPEMBEDZO
Anakhaladi ndi Moyo Wautali Choncho? (anthu amene anakhalako chigumula chisanachitike), 7/07
Baibulo Lakumana ndi Zambiri, 11/07
Baibulo ndi Umboni Wosatha wa Chikondi cha Mulungu, 11/07
Buku Lapadera (Baibulo), 11/07
Chingalawa cha Nowa Chinapangidwa Mwaluso, 1/07
Imfa ndi Mapeto a Zonse? 12/07
Kodi Baibulo Limanena za Chiyani? 11/07
Mulungu ndi Amene Amachititsa Masoka Achilengedwe? 9/07
Ndalama Zinafalitsa Dzina la Mulungu, 12/07
Nyumba Zobatiziramo Anthu, 9/07
Tiyenera Kukhulupirira Baibulo? 11/07
Zikutha Mphamvu? 2/07
Zoona Kapena Zopeka? (zimene Baibulo limaphunzitsa), 11/07
CHUMA NDI NTCHITO
Kukonda Ndalama, 6/07
MAUNANSI A ANTHU
Kuthandiza Achinyamata Kupeza Zomwe Amafunikira, 3/07
Mfundo Zolerera Bwino Ana, 8/07
Mungateteze Ana Anu (kwa ogona ana), 10/07
“Sonyezani Kuti Ndinu Oyamikira,” 10/07
Zolumbira Kukhala Wodzisunga, 2/07
MAYIKO NDI ANTHU
Akatswiri Ochapa Zovala ku Abidjan (Côte d’Ivoire), 6/07
Amwenye a ku Brazil, 10/07
Baikal, Ndi Nyanja Yaikulu Kwambiri padziko Lonse (Russia), 12/07
Chilumba cha Kamchatka ku Russia N’chochitsa Kaso, 3/07
Chilumba Chotchedwa Christmas Island, 8/07
Gombe la Shark Bay (Australia), 7/07
Kodi Mungadye Mbozi? (Zambia), 5/07
Kuchoka ku Iguputo Kupita ku Mizinda Yambiri Padzikoli (zipilala), 4/07
Kum’mawa kwa Timor, 5/07
Malo a Zachilengedwe, 1/07
Maluwa Okongola Mokopa a Kuno ku Africa, 10/07
“Mbalame ya Chinsansa” mu Ngalande za ku Venice (Italy), 5/07
Mfumu Imene Inachita Zazikulu (Cameroon), 12/07
Mfumu Imene Inafunafuna Nzeru (Spain), 1/07
Mkokomo wa “Mzinda wa Muyaya” (Trevi Fountain, Rome), 8/07
“Nzeru za M’chilengedwe” (Expo 2005, Japan), 3/07
Svalbard Dera Lozizira la Mphepete mwa Nyanja (Norway), 2/07
Thanthwe Lochititsa Chidwi (Canada), 4/07
Toledo (Spain), 6/07
Vanuatu, 9/07
Zauchigawenga ku Mumbai (India), 6/07
Zombo za Nkhondo za ku Spain, 8/07
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Chinthu Chokhalitsa Kuposa Luso la Zosemasema ndi Zoumbaumba (R. Koivisto), 4/07
Mafunde Sangapose Zimenezi Ngakhale Atatalika Motani (K. H. Schwoerer), 12/07
Ndimakonda Nyimbo, Moyo, ndi Baibulo (B. Gulashevsky), 8/07
Ndinasankha Mwanzeru (S. Quevedo), 3/07
Sindinenso Kapolo wa Mowa, 5/07
“Yehova, Ndiloleni Kuti Ndikutumikireni” (D. Hall), 7/07
Zimene Zinandisiyitsa Moyo Wotchuka (M. Neím), 6/07
MBONI ZA YEHOVA
“Athandiza Kwambiri Pazachipatala (mankhwala opanda magazi), 9/07
Kodi Chifuno cha Moyo N’chiyani? 8/07
Nyanja ya Baikal (Russia), 12/07
Nyumba ya Mphamvu za Magetsi Iyamba Kuwala Mwauzimu (Nyumba ya Ufumu, ku Italy), 10/07
“Tsatirani Khristu!” Msonkhano Wachigawo, 5/07, 6/07
Ubwino Wophunzitsa Ana Anu Mawu a Mulungu, 8/07
SAYANSI
Nthenga, 7/07
Vuto Losiyanitsa Mitundu, 7/07
Zinthu Zakale Zimasonyeza Kuti Baibulo ndi Lolondola, 11/07
UMOYO NDI MANKHWALA
“Athandiza Kwambiri Pazachipatala” (mankhwala opanda magazi), 9/07
Bwanji Ndimakomokakomoka? 4/07
Kusangalala, 9/07
Matenda Onse Adzatha! 1/07
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kukaonana ndi Dokotala wa Mano? 5/07
Vuto la Mano, 9/07
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Bwanji Ngati Wina Atandifunsira Kuti Tikagonane? 3/07
Kodi Ndingapewe Bwanji Khalidwe Lofuna Kugonana ndi Amuna Kapena Akazi Anzanga? 2/07
Kodi Ndingapewe Bwanji Kuona Zithunzi Zolaula? 12/07
Kodi Ndingapewe Bwanji Miseche? 8/07
Kodi Nditsatire Chikhalidwe Chiti? 9/07
Kuchita Chibwenzi Mobisa, 6/07
Makolo Akamakangana, 10/07
Munthu Ameneyu Ndi Woyenera Kumanga Naye Banja? 5/07
N’chifukwa Chiyani Anthu Amakonda Kundifananitsa ndi Ena? 4/07
N’chifukwa Chiyani Ndimasowa Anthu Ocheza Nawo? 7/07
Ndingayambe Chibwenzi Titafika Msinkhu Wotani? 1/07
Ndizitsatira Mfundo za m’Baibulo Chifukwa Chiyani? 11/07
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Chikhristu Chalephera, 1/07
Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira? 10/07
Kodi Kukhala Mkhristu Kumatanthauza Chiyani? 4/07
Kodi Kulambira Mulungu Kungakhale Kosangalatsa? 8/07
Kodi Mlembi wa Baibulo Ndani? 11/07
Kudzichepetsa ndi Mantha Kapena N’chamuna? 3/07
Kudziona Ndalama Moyenera, 6/07
“Kukhala Wabwino,” 7/07
Mulungu Analemberatu Tsogolo Lanu? 5/07
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusamalira Chilengedwe? 12/07
N’kulakwa Kugwiritsa Ntchito Njira Zakulera? 9/07
Satana Alikodi? 2/07
ZINYAMA NDI ZOMERA
Gombe Lochititsa Chidwi la Shark Bay, 7/07
Kachilombo Kam’madzi (kamayenda pang’onopang’ono), 3/07
Kodi Mungadye Mbozi? (malasankhuli), 5/07
Maluwa Okongola Mokopa a Kuno ku Africa, 10/07
Mbalame Zimatsogoleredwa ndi Nzeru Zachibadwa, 7/07
Misondozi, 2/07
Mungu, 4/07
Nkhwali (mbalame), 2/07
Nsomba, 10/07
Opanga Mafuta Onunkhira Amakonda Chipatsochi, 6/07
Tizakudya Tokoma Tam’tchire (zipatso), 9/07
Zikumbu (ladybug), 1/07
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Ananeneratu za “Zipangizo Zosakazira Anthu” (ndenge zonyamula zida zankhondo), 10/07
Makhalidwe Akulowa Pansi, 4/07
Mavuto a Kuchuluka kwa Magalimoto Pansewu, 2/07
M’dziko Lokondera, 5/07
ZOSIYANASIYANA
Chimphona Chimene Chili Mtulo, (kuphulika), 2/07
Kunika Nsalu, 4/07
Kuphunzira Chinenero China, 3/07
Kutsogoleredwa ndi Nzeru Zapamwamba Kuposa Zachibadwa, 7/07
Pensulo, 7/07