Dziwani Zambiri pa JW.ORG
Kodi ndi nkhani iti imene mukufuna kuidziwa bwino?
Mmene ndingalimbitsire banja langa
Onani nkhani yakuti “Kodi Mungatani Kuti Zipangizo Zamakono Zisamakusokonezeni?”
Mmene ndingaphunzitsire ana anga makhalidwe abwino
Onani nkhani yakuti “Phunzitsani Ana Anu Kugwiritsa Ntchito Foni Mosamala.”
Mmene ndingachepetsere kuda nkhawa ndi zinthu zam’tsogolo
Onani nkhani ya pachikuto ya mutu wakuti “Kodi M’tsogolomu Muli Zotani?”
Baibulo lingakuthandizeni inuyo komanso banja lanu kuti muzikhala ndi moyo wabwino panopa komanso kuti mukhale ndi chiyembekezo chodalirika cha zinthu zam’tsogolo.