Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2016
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
Kodi anthu a Mulungu analowa liti mu ukapolo wa m’Babulo Wamkulu? Mar.
Kodi odzozedwa amalandira bwanji “chikole” nanga amadindidwa bwanji “chidindo”? (2 Akor 1:21, 22), Apr.
Kodi Satana anapitadi ndi Yesu kukachisi? (Mat. 4:5; Luka 4:9), Mar.
Kupereka ndalama kwa ogwira ntchito m’boma, May
Kusangalala munthu akabwezeretsedwa, May
“Mawu a Mulungu” pa Aheberi 4:12, Sept.
Munthu wa kachikwama konyamulira inki ndi amuna 6 okhala ndi zida (Ezek. 9:2), June
Nkhani ya kusamba m’manja (Maliko 7:5), Aug.
MBIRI YA MOYO
Kukhala “Zinthu Zonse kwa Anthu Osiyanasiyana” (D. Hopkinson), Dec.
Masisitere Anasintha N’kukhala Alongo (F. ndi A. Fernández), Apr.
Ndilibe Manja Koma Ndinalandira Choonadi (B. Merten), Na. 6
Ndimasangalala Chifukwa Chothandiza Ena (R. Parkin), Aug.
Ndimayesetsa Kutengera Anthu a Zitsanzo Zabwino (T. McLain), Oct.
Yehova Wandithandiza Kwambiri Pomutumikira (C. Robison), Feb.
MBONI ZA YEHOVA
Anadzipereka ndi Mtima Wonse, ku Ghana, July
Anadzipereka ndi Mtima Wonse, ku Oceania, Jan.
Galimoto Yodziwika Yokhala ndi Zokuzira Mawu (Brazil), Feb.
“Kwa Amene Apatsidwa Ntchitoyi” (msonkhano wachigawo wa ku Cedar Point, Ohio, U.S.A.), May
Muzilola Kuti Yehova Azikutsogolerani (zomwe zinachitikira a Mboni ena), Sept.
“Ndikugwira Ntchito Yotamanda Yehova” (Germany, nkhondo yoyamba ya padziko lonse), Aug.
“Ntchitoyi Ndi Yaikulu” (zopereka), Nov.
“Ofalitsa a ku Britain Galamukani!” (1937), Nov.
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Anateteza Uthenga Wabwino kwa Akuluakulu a Boma, Sept.
Chuma Chamtengo Wapatali Kuposa Golide (nzeru zochokera kwa Mulungu), Aug.
Khalidwe la Mtengo Wapatali Kuposa Dayamondi (kuona mtima), June
Kodi Utumiki Wanu Uli Ngati Mame? Apr.
Kupemphera mu Akachisi? Na. 2
Luso Loona Zinthu M’maganizo Mwathu, Apr.
‘Mumasunga Nzeru Zopindulitsa’? Oct.
Mungatani Kuti Muzitumikirabe Yehova Mosangalala, Feb.
Mungathandize Bwanji Mpingo Wanu? Mar.
Munthu Wofatsa Amasonyeza Nzeru, Dec.
Musamade Nkhawa, Na. 1
Musamakhale Mwamantha, Na. 1
Muzitsanzira Aneneri, Mar.
Kuchita Zinthu Moona Mtima? Na. 1
NKHANI ZOPHUNZIRA
Abulahamu Anali “Bwenzi” la Yehova,” Feb.
Achinyamata, Kodi Mungakonzekere Bwanji Kubatizidwa? Mar.
Achinyamata, Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa? Mar.
Achinyamata, Yesetsani Kulimbitsa Chikhulupiriro Chanu, Sept.
Anatuluka mu Babulo Wamkulu, Nov.
Anthu a Mulungu Anaitanidwa Kuchoka Mumdima, Nov.
Kodi Baibulo Likusinthabe Moyo Wanu? May
Kodi Kuphunzitsa Ena N’kofunika Bwanji? Aug.
Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu? Sept.
Kodi Mumalola Kuti Yehova Azikuumbani? June
Kodi Mumaona Kuti Baibulo Ndi Buku Lapadera? Nov.
Kodi Mumasankha Bwanji Zochita? May
Kodi Mumathetsa Nkhani Mwachikondi Mukasemphana Maganizo? May
Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino? Aug.
Kodi Tingatani Kuti Tizichita Zambiri M’gulu la Yehova? Aug.
Kodi Tingathandize Bwanji Kulimbitsa Mgwirizano Wathu? Mar.
Kodi Ukwati Unayamba Bwanji Nanga Cholinga Chake N’chiyani? Aug.
Kodi Zinthu Zonse Zimene Yehova Amatipatsa Zimakuthandizani? May
‘Kuika Maganizo pa Zinthu za Mzimu Kumabweretsa Moyo ndi Mtendere,’ Dec.
Manja Anu ‘Asalefuke,’ Sept.
Mawu a Mulungu Amatithandiza Kuti Tizichita Zinthu Mwadongosolo, Nov.
“Mulole Kuti Kupirira Kumalize Kugwira Ntchito Yake,” Apr.
Mungatani Kuti Mukhalebe Olimba Mwauzimu Mumpingo wa Chilankhulo China? Oct.
“Mupitirize Kukonda Abale,” Jan.
“Musaiwale Kuchereza Alendo,” Oct.
Musakhale Mbali ya Dzikoli, Apr.
Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina, July
Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova, Feb.
Muzikhulupirira Kwambiri Zinthu Zimene Mukuyembekezera, Oct.
Muzimutulira Yehova Nkhawa Zanu Zonse, Dec.
Muzisonyeza Kuti Mumakhulupirira Malonjezo a Yehova, Oct.
Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale ndi Chikhulupiriro Cholimba, , Sept.
Mzimu Umachitira Umboni Limodzi ndi Mzimu Wathu, Jan.
N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhalabe Maso’? July
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana? Apr.
“Pitani Mukaphunzitse Anthu a Mitundu Yonse,” May
Pitirizani Kulimbana ndi Zimene Zingakulepheretseni Kupeza Madalitso, Sept.
Timasangalala Kwambiri Kugwira Ntchito Limodzi ndi Mulungu, Jan.
Tinamasulidwa ku Uchimo Chifukwa cha Kukoma Mtima Kwakukulu, Dec.
“Tipita Nanu Limodzi,” Jan.
Tipitirize Kulimbikitsana Tsiku ndi Tsiku, Nov.
Tisasiye Kutumikira Yehova Chifukwa cha Zochita za Ena, June
Tizilalikira Uthenga wa Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu, July
Tiziyamikira ‘Mphatso Yaulere’ Imene Mulungu Anatipatsa, Jan.
Tiziyamikira Kukoma Mtima Kwakukulu kwa Mulungu, July
Tiziyamikira Kuti Yehova Amatiumba, June
Tsanzirani Anthu Amene Anali pa Ubwenzi Wolimba ndi Yehova, Feb.
Tsanzirani Atumiki a Yehova Amene Anali Okhulupirika, Feb.
Yehova Amadalitsa Anthu Okhulupirika, Apr.
Yehova Amapereka Mphoto kwa Anthu Omufunafuna ndi Mtima Wonse, Dec.
Yehova Amatsogolera Anthu Ake Kuti Adzapeze Moyo, Mar.
“Yehova Mulungu Wathu ndi Yehova Mmodzi,” June
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Ansembe Aakulu M’Malemba Achigiriki, Na. 1
Aroma Ankapereka Ufulu kwa Ayuda a ku Yudeya, Oct.
Atsogoleri Achipembedzo Chachiyuda Ankalola Munthu Kuthetsa Ukwati pa Zifukwa Ziti? Na. 4
“Inde Ndipita” (Rabeka), Na. 3
Kodi Anthu Anayambitsa Kupembedza? Na. 4
Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira? Na. 1
Kodi Mdyerekezi ndi Ndani? Na. 2
Kodi Mungayerekezere Zomwe Mumakhulupirira Ndi Zimene Baibulo Limaphunzitsa? Na. 4
Kodi Munthu Ankafesadi Namsongole M’munda wa Mnzake? Oct.
Kodi Munthu Ayenera Kukhala M’chipembedzo Chinachake? Na. 4
Kodi Ndani Angatithandize Tikakhala pa Mavuto? Na. 5
Kodi Nkhani ya Davide ndi Goliyati Inachitikadi? Na. 5
Kodi Tiyenera Kukhala Mwanjira Inayake Popemphera? Na. 6
Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Na. 5
Kodi Zachiwawa Zidzatha Padzikoli? Na. 4
Kumvera Chenjezo, Na. 2
Masomphenya Osonyeza Amene Ali Kumwamba, Na. 6
Mawu Olimbikitsa Kwambiri! (“mwana wanga”), Nov.
Mipukutu Yakale, Na. 1
Mulungu Amayankha Mapemphero Onse? Na. 6
Munthu Yemwe Munkamukonda Akamwalira, Na. 3
Utoto Komanso Nsalu Zimene Anthu Akale Ankagwiritsa Ntchito, Na. 3
“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo” (Davide), Na. 5
Zimene Tingaphunzire kwa Mbalame, Na. 6
YEHOVA