Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2017
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
Kodi Akhristu angagwiritse ntchito lupu (IUD) ngati njira ya kulera? Dec.
Kodi mwana woyamba kubadwa ndi amene ankakhala mumzere wa makolo a Mesiya? Dec.
Kodi ndi nzeru kuti Mkhristu azisunga mfuti pofuna kudziteteza kwa anthu? July
N’chifukwa chiyani nkhani zokhudza moyo wa Yesu ali mwana zimene Mateyu ndi Luka analemba zimasiyana? Aug.
Yehova “sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire” (1Akor. 10:13), Feb.
MBIRI YA MOYO
Kuyenda ndi Anthu Anzeru Kwandithandiza Kwambiri (W. Samuelson), Mar.
Mulungu Anatisonyeza Kukoma Mtima Kwakukulu M’njira Zambiri (D. Guest), Feb.
Ndakhala ndi Mwayi Wotumikira Limodzi ndi Abale Okhulupirika (D. Sinclair), Sept.
Ndinasiya Zinthu Zambiri Kuti Nditsatire Ambuye (F. Fajardo), Dec.
Ndine Msilikali wa Khristu (D. Psarras), Apr.
Tikapirira Mavuto Tidzadalitsidwa (P. Sivulsky), Aug.
Timadalitsidwa Tikamachita Zimene Yehova Amatiuza (O. Matthews), Oct.
Vuto Losamva Silinandilepheretse Kuphunzitsa Anthu Ena Baibulo (W. Markin), May
MBONI ZA YEHOVA
Anadzipereka ndi Mtima Wonse (alongo osakwatiwa), Jan.
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Turkey, July
Anamusonyeza Kukoma Mtima, Oct.
Kodi Mungatani Kuti Muzolowere Mpingo Wanu Watsopano? Nov.
“Kodi Tichitanso Liti Msonkhano Wina?” (Mexico), Aug.
‘Kukonda Kwambiri Yehova Ndiponso Kulalikira Mwakhama’ (msonkhano wa 1922), May
“Kungatalike Bwanji Ndipo Msewu Ungaipe Bwanji Ankafikako” (Australia), Feb.
Moyo Wosalira Zambiri Ndi Wosangalatsa, May
“Munthu Wopatsa Adzadalitsidwa” (zopereka), Nov.
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Chikondi Ndi Khalidwe Lamtengo Wapatali Kwambiri, Aug.
Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Khirisimasi? Na. 6
Kodi Atumiki Achikhristu Safunika Kukwatira? Na. 2
Kodi Mumakhalabe Bwenzi Labwino Zinthu Zikavuta? Mar.
Kodi Mumathetsa Kusamvana N’kukhazikitsa Mtendere? June
Kodi Tizitani Tikalakwitsa Zinthu? Na. 6
Tetezani Maganizo Anu, July
Ubwino wa Mtima Wopatsa, Na. 2
NKHANI ZOPHUNZIRA
Achinyamata “Pitirizani Kukonza Chipulumutso Chanu,” Dec.
Cholinga cha Yehova Chidzakwaniritsidwa, Feb.
Choonadi Sichibweretsa “Mtendere Koma Lupanga,” Oct.
Dipo Ndi ‘Mphatso Yangwiro’ Yochokera kwa Atate, Feb.
“Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino,” Jan.
Kodi Masomphenya a Zekariya Akukukhudzani Bwanji? Oct.
Kodi Mukhoza Kuyembekezera Moleza Mtima? Aug.
Kodi Mumathawira kwa Yehova? Nov.
Kodi Mumatsanzira Yehova pa Nkhani ya Chilungamo? Apr.
Kodi Mumatsatira Ndi Mtima Wonse Zimene Zinalembedwa? Mar.
Kodi Ndi Ndani Akutsogolera Anthu a Mulungu Masiku Ano? Feb.
Kodi Tingatani Kuti Nthawi Zonse Tizikhala Odzichepetsa? Jan.
Kodi Tingathandize Bwanji Ana a Anthu Ochokera M’mayiko Ena? May
Kodi Ufumu wa Mulungu Ukadzabwera Udzachotsa Zinthu Ziti? Apr.
“Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?” May
Kudzichepetsa N’kofunika Kwambiri, Jan.
Kudzipereka Kwathu Kumachititsa Kuti Yehova Atamandidwe, Apr.
‘Limba Mtima Ndipo Ugwire Ntchitoyi,’ Sept.
“Lirani ndi Anthu Amene Akulira,” July
‘Mawu a Mulungu Ndi Amphamvu,’ Sept.
“Mawu a Mulungu Wathu Adzakhala Mpaka Kalekale,” Sept.
‘Mtendere wa Mulungu Umaposa Kuganiza Mozama Kulikonse,’ Aug.
‘Mulungu Akwaniritse Zofuna Zanu,’ July
Musalole Kuti Chikondi Chanu Chizirale, May
Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni Kulandira Mphoto, Nov.
Musamaiwale Nkhani Yofunika Kwambiri, June
Muzifunafuna Chuma Chenicheni, July
Muzikhala Kumbali ya Ulamuliro wa Yehova, June
Muzikhulupirira Yehova Kuti Muzisankha Zochita Mwanzeru, Mar.
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutamanda Yehova? July
“Ndikudziwa Kuti Adzauka,” Dec.
“Ndili ndi Chiyembekezo mwa Mulungu,” Dec.
Pewani Kutengera Maganizo a M’dzikoli, Nov.
Thandizani Ana Anu Kupeza Nzeru Kuti Adzapulumuke, Dec.
Timatetezedwa ndi Magaleta Komanso Chisoti Chachifumu, Oct.
Tiziimba Mosangalala, Nov.
Tizikonda ndi Mtima Wonse Chuma Chimene Mulungu Watipatsa, June
Tizipereka Ulemu kwa Oyenera Kulemekezedwa, Mar.
“Tizisonyezana Chikondi Chenicheni M’zochita Zathu,” Oct.
Tizithandiza Alendo Kuti ‘Azitumikira Yehova Mokondwera,’ May
Tizitsanzira Yehova pa Nkhani ya Chifundo, Sept.
Tizitumikira Yehova ndi Mtima Wathunthu, Mar.
Tiziyesetsa Kukhala Odziletsa, Sept.
Tsanzirani Chilungamo ndi Chifundo cha Yehova, Nov.
Ufulu Wosankha Zochita Ndi Mphatso Yapadera, Jan.
“Uzikwaniritsa Zinthu Zimene Walonjeza,” Apr.
Valani Umunthu Watsopano Ndipo Musauvulenso, Aug.
“Woweruza wa Dziko Lonse Lapansi” Amachita Zachilungamo, Apr.
Yehova Amatitonthoza M’masautso Athu Onse, June
Yehova Amatsogolera Anthu Ake, Feb.
Zimene Zinawathandiza Kuvula Umunthu Wakale, Aug.
‘Zinthu Zimenezo Uziziphunzitsa kwa Anthu Okhulupirika,’ Jan.
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Akapolo Anapeza Ufulu, Na. 2
Anthu 4 Okwera Pamahatchi, Na. 3
Dzina la M’Baibulo Pamtsuko Wakale, Mar.
Kachilembo Kachiheberi, Na. 4
Kodi Amalonda Amene Ankagulitsa Nyama Kukachisi Analidi Ngati “Achifwamba?” June
Kodi Angelo Angakuthandizeni? Na. 5
Kodi Ayuda Anali ndi Chizolowezi Chotani Chomwe Chinachititsa Yesu Kuuza Anthu Kuti Asamalumbire? Oct.
Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Imfa? Na. 4
Kodi Dzikoli Lidzakhaladi Paradaiso Kapena Ndi Maloto Chabe? Na. 4
Kodi Gayo Ankathandiza Bwanji Akhristu Anzake? May
Kodi Kale Anthu Ankanyamula Bwanji Moto? Jan.
Kodi Padzikoli Padzakhaladi Mtendere? Na. 5
Kodi Tili ‘M’masiku Otsiriza’? Na. 2
Kuvutika, Na. 1
Malangizo Amene Paulo Anapereka Okhudza Ulendo (Mac. 27), Na. 5
Mphatso Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse, Na. 6
‘Mulungu Anakondwera Naye’ (Inoki), Na. 1
Mungatani Ngati Munthu Amene Mumamukonda Akudwala Matenda Oti Sachira? Na. 4
“Ndiwe Mkazi Wokongola” (Sara), Na. 3
Nkhawa, Na. 4
Tisamaweruze Anthu Chifukwa cha Maonekedwe Awo, June
“Udalitsike Chifukwa cha Kulingalira Bwino Kwako” (Abigayeli), June
Yehova Anamutchula Kuti “Mfumukazi” (Sara), Na. 5
Yosefe wa ku Arimateya, Oct.