Mlozerankhani Wa Nkhani Za M’magazini A Nsanja Ya Olonda A 2004
Mlozerankhani Wa Nkhani Za M’magazini A Nsanja Ya Olonda A 2004
Wosonyeza deti la magazini yopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
‘Anayendayenda Kufalitsa Uthenga Wabwino’ (G. Borrow), 8/15
Chuma cha Chester, 9/15
Complutensian Polyglot, 4/15
“Lomasuliridwa Bwino Kwambiri” (New World Translation), 12/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Genesis—I, 1/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Genesis—II, 1/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Eksodo, 3/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Levitiko, 5/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Numeri, 8/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Deuteronomo, 9/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Yoswa, 12/1
KALENDALA
Chuma Chochuluka cha M’nyanja, 9/15
Malimwe ndi Dzinja Sizidzatha, 7/15
“Mitengo ya Mulungu Yadzala ndi Madzi,” 1/15
‘Mitsinje Iombe M’manja,’ 5/15
“Ntchito Zanu Zichulukadi!” 11/15
‘Wamkulu Kuposa Mapiri,’ 3/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Aisrayeli amene anaphedwa anali 23,000 kapena 24,000? (1Akor. 10:8; Num. 25:9), 4/1
Chifukwa chake amuna achiisrayeli ankaloledwa kukwatira akazi amene anawagwira ukapolo, 9/15
Chifukwa chake Yesu analola Tomasi kum’khudza pamene analetsa Mary wa Magadala kutero, 12/1
Hanameli anagulitsa bwanji munda kwa Yeremiya? (Yer. 32:7), 3/1
‘Kongoletsani osayembekeza kanthu konse’ (Luka 6:35), 10/15
Kususuka, 11/1
Nambala ya 144,000 ndi yeniyeni? 9/1
N’chifukwa chiyani Mikala anali ndi terafi? (1Sam. 19:13), 6/1
N’chifukwa chiyani Yuda anagona ndi mkazi amene ankamuyesa wadama? (Gen. 38:15), 1/15
N’chiyani chinachitika ndipo ndani akanaphedwayo? (Eks. 4:24-26), 3/15
Ngalawa imene Paulo anakwera inaswekera ku Melita? 8/15
Ngamila ndi singano zenizeni? (Mat. 19:24; Mk. 10:25; Luka 18:25), 5/15
Njiwa inakatenga kuti tsamba la azitona? (Gen. 8:11), 2/15
‘Osakhulupirira’ (2 Akor. 6:14), 7/1
‘Satana analinkugwa kuchokera kumwamba’ (Luka 10:18), 8/1
Tingamvetse chisoni motani mzimu woyera? (Aef. 4:30), 5/15
Tizigawo tating’ono totengedwa m’magazi, 6/15
Zimene Chaka Choliza Lipenga chimasonyeza za m’tsogolo, 7/15
Ziwanda pa nthawi ya Zaka 1,000, 11/15
MBIRI YA MOYO WANGA
Kuchoka M’ndende Zamdima Kupita ku Mapiri a ku Switzerland (L. Walther), 6/1
Kudalira Chisamaliro cha Yehova (A. Denz Turpin), 12/1
Kukhala Wokhutira ndi Zimene Mulungu Wandipatsa Kwandithandiza (I. Osueke), 3/1
Kusankha Ulamuliro wa Mulungu Mosasunthika (M. Žobrák), 11/1
Maphunziro Amene Ndikupitirizabe Mpaka Pano (H. Gluyas), 10/1
Maso Anatseguka Ngakhale Kuti Ndinali Wakhungu! (E. Hauser), 5/1
Moyo Wanga Wosangalatsa Ngakhale Ndakumana N’zachisoni (A. Hyde), 7/1
Pamoyo Wathu Takhala Tikudalira Mphamvu za Yehova (E. Haffner), 8/1
Tadalitsidwa Chifukwa Chodzimana (G. Aljian), 4/1
Tadalitsidwa Kwambiri Chifukwa Chokhala ndi Mtima Waumishonale (T. Cooke), 1/1
Takhala ndi Moyo Watanthauzo Chifukwa Chodzipereka (M. and R. Szumiga), 9/1
Yehova Anandikomera Mtima (F. King), 2/1
MBONI ZA YEHOVA
‘Anatiphunzitsa Kulemekeza Chipembedzo Chake’ (Italy), 6/15
Anauzako Anthu Am’kalasi Zimene Amakhulupirira (Poland), 10/1
Chikukula, 3/1
Chikumbumtima Chokoma (anabweza telefoni ya m’manja), 2/1
Kalata Yochokera kwa Alejandra (Mexico), 10/1
Kuchita Chokoma Panthaŵi ya Mavuto, 6/1
Kudalitsidwa Chifukwa Chopatsa (zopereka), 11/1
Kukumbukira “Anthu Oiwalika Amene Anazunzidwa,” 9/1
Kulalikira Anthu ku Ntchito, 4/1
Kulalikira Mwamwayi M’gawo la Chingelezi ku Mexico, 4/15
Kusonkhana pa ‘Mchombo wa Dziko’ (Chilumba cha Easter), 2/15
Liberia, 4/1
Misonkhano Yachigawo Yakuti “Patsani Mulungu Ulemerero,” 1/15
Misonkhano Yachigawo Yakuti “Yendani ndi Mulungu,” 3/1
‘Muwolokere Kuno Mudzathangate’ (Bolivia), 6/1
Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15
Okhulupirika Ndiponso Osasunthika (Poland), 10/15
Olankhula Zinenero Zamakolo ku Mexico, 8/15
Si Maseŵera Chabe (ana), 10/1
Zisumbu za Tonga, 12/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Abrahamu ndi Sara Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo! 5/15
Achinyamata Lolani Kuti Makolo Akuthandizeni Kuteteza Mtima! 10/15
Chitonthozo kwa Ovutika, 2/15
‘Hema wa Oongoka Mtima Adzakula’ (Miy. 14), 11/15
Kudikira M’njira Yoyenera, 10/1
Kukonzera Ana Cholowa, 9/1
Kulimbana ndi Kutaya Mtima, 9/1
Kulimbana ndi Vuto la Kusatsimikizika kwa Zinthu, 2/1
Kuphunzitsa Ana, 6/15
Kusaloŵerera M’ndale Kumalepheretsa Kusonyeza Chikondi? 5/1
Kuyang’ana pa Mphoto, 4/1
‘Limba Nayoni Nkhondo Yabwino ya Chikhulupiriro,’ 2/15
Mavuto Amalamulira Moyo Wanu? 6/1
Mgonero wa Ambuye, 3/15
Mmene Timasonyezera Kuti Timakonda Mulungu, 3/1
Mungatani Kuti Mudziwe Choyenerera ndi Chosayenerera? 12/1
‘Wochenjera Amachita Mwanzeru’ (Miy. 13), 7/15
Zolinga Zauzimu, 7/15
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
Achinyamata, Kodi Mukukonzekera Tsogolo? 5/1
“Ambuye, Tiphunzitseni Ife Kupemphera” (Pemphero Lachitsanzo), 2/1
Anthu a Yehova Ayenera Kukonda Khalidwe la Kukoma Mtima, 4/15
Anthu Onse Alengeze Ulemerero wa Yehova, 1/1
‘Aphunzitseni Kusunga Zinthu Zonse Zimene Ndinakulamulirani,’ 7/1
Atumiki Achimwemwe a Yehova, 11/1
Chenjerani ndi “Mawu a Alendo,” 9/1
Chikondi Chokhulupirika cha Yehova N’chachikulu, 1/15
Chilengedwe Chimalengeza Ulemerero wa Mulungu! 6/1
‘Chitani Ntchito ya Mlaliki wa Uthenga Wabwino,’ 3/15
Dalirani Mzimu wa Mulungu Zinthu Zikasintha pa Moyo Wanu, 4/1
Funafunani Yehova, Amene Amayesa Mitima, 11/15
Kanizani Mzimu wa Dziko Lomwe Likusinthali, 4/1
“Kapolo” Amene Ali Wokhulupirika ndi Wanzeru, 3/1
“Kapolo Wokhulupirika” Wapambana Mayeso! 3/1
Khalani ndi Maganizo a Kristu Pankhani ya Kukhala Wamkulu, 8/1
Khalanibe Odzisunga mwa Kutchinjiriza Mtima Wanu, 2/15
Khalani Wolimba Mtima Ngati Yeremiya, 5/1
Kukhala Okoma Mtima M’dziko Losaganiziranali, 4/15
Kusamalira Okalamba Ndi Udindo wa Akristu, 5/15
‘Kwaniritsani Utumiki Wanu,’ 3/15
Lankhulani Mawu a Mulungu Molimba Mtima, 11/15
Lemekezani Mulungu ndi ‘Pakamwa Pamodzi,’ 9/1
“Liwu Lawo Linatulukira ku Dziko Lonse Lapansi,” 1/1
‘Maonekedwe a Dzikoli Akusintha,’ 2/1
Mowa Umafunika Kusamala Nawo, 12/1
“Mukani, Phunzitsani,” 7/1
“Mukondane ndi Chikondi Chaubale,” 10/1
Muli ndi Chifukwa Chomveka Choyembekezera Paradaiso? 10/15
Mumakondwera ndi ‘Chilamulo cha Yehova’? 7/15
Mumalola Kuti Yehova Akuthandizeni? 12/15
Ndani Amene Akupatsa Mulungu Ulemerero Masiku Ano? 10/1
Odala Ndi Amene Amapatsa Mulungu Ulemerero, 6/1
Odedwa Popanda Chifukwa, 8/15
Okalamba Ndi Ofunika Kwambiri pa Ubale Wathu Wachikristu, 5/15
Onani Mphatso ya Moyo Wanu Kuti Ndi Yamtengo Wapatali, 6/15
Otopa Koma Osalefuka, 8/15
Ozunzidwa Komabe Achimwemwe, 11/1
Peŵani Chinyengo, 2/15
“Tadzilimbikani mwa Ambuye,” 9/15
Tonthozanani, 5/1
Tsatirani Malangizo a Mulungu Wamoyo, 6/15
Ukulu wa Yehova Ndi Wosasanthulika, 1/15
Yehova Adzaweruza Oipa, 11/15
Yehova Amaonetsa Ulemerero Wake kwa Odzichepetsa, 8/1
Yehova Amatipatsa Zimene Timafunikira Tsiku Lililonse (Pemphero Lachitsanzo), 2/1
Yehova Ndiye ‘Linga Lathu M’nyengo ya Nsautso,’ 8/15
Yehova Ndiye Mthandizi Wathu, 12/15
Yendani mu Umphumphu, 12/1
‘Yendayenda M’dzikoli,’ 10/15
“Zida Zonse za Mulungu,” 9/15
‘Zimene Yehova Watsimikiza’ Sizingalephereke, 7/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
666—Si Nambala Yongodabwitsa Chabe, 4/1
“Anapita M’ngalawa ku Kupro,” 7/1
Atsogoleri a Zipembedzo Aziloŵerera M’ndale? 5/1
Atumiki a Mulungu Ali Ngati Mitengo, 3/1
Boma Labwino, 8/1
Boma la Ufumu Likuchita Zooneka, 8/1
Chilombo ndi Chizindikiro Chake, 4/1
Chimwemwe, 9/1
Chipembedzo Ndicho Chikuchititsa Mavuto? 2/15
Ehudi, 3/15
Gulu la Anabaptist, 6/15
“Imodzi Mwa Ntchito Zimene Panagona Luso Kwambiri” (Thaŵale Lamkuwa), 1/15
Kalata Yopita kwa Nowa, 7/1
Kapadokiya, 7/15
Kukonda Zinthu Zauzimu Kumakhudza Moyo, 2/1
Kulambira Koona ndi Uchikunja Zinalimbana (Efeso), 12/15
Kupeza Malangizo Abwino, 8/15
Mapemphero Angasinthitse Zinthu? 6/15
Maseŵera Akale, 5/1
Matchalitchi Apulumuka Mavuto Awo? 3/1
“Mulungu Woona ndi Moyo Wosatha” (1 Yoh. 5:20), 10/15
Mumafuna Kukhala ndi Moyo Wosatha? 11/15
Mungadalire Malonjezo a Ndani? 1/15
Muyenera Kukhala M’chipembedzo Chinachake? 6/1
N’chiyani Chimapangitsa Moyo Kukhala ndi Cholinga Chenicheni? 8/1
“Ofatsa Choloŵa Chawo ndi Dziko Lapansi,” 10/1
Pangano la Mtendere la ku Westphalia, 3/15
Pemphero la Ambuye, 9/15
Rebeka, 4/15
Tingayembekezere Mtendere, 1/1
Tiyenera Kupemphera kwa Angelo Kuti Atithandize? 4/1
Utsogoleri Wabwino, 11/1
Zinthu Zauzimu, 10/15
Zinthu Zauzimu Zimene Mumafunikira, 2/1
Zogayira Chakudya Chathu, 9/15
YEHOVA
Amakuganizirani, 7/1
Amatiganizira? 1/1
Kudzichepetsa, 11/1
‘Kufuna Kwanu Kuchitidwe Pansi Pano,’ 4/15
Kukondweretsa Mulungu? 5/15
“Ntchito Zanu Zichulukadi!” 11/15
YESU KRISTU
Kubadwa Kwake N’koyenera Kukukumbukira, 12/15
Zozizwitsa Zinali Zenizeni Kapena Nthano Chabe? 7/15