NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) July 2013

Magaziniyi ikusintha zinthu zambiri zimene tinkakhulupirira zokhudza nthawi imene ulosi wa Yesu uyenera kukwaniritsidwa ndiponso zokhudza kapolo wokhulupirika ndi wanzeru.

“Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzachitika Liti?”

Kodi tasintha zinthu ziti zimene tinkakhulupirira pa ulosi wa Yesu wa pa Mateyu chaputala 24 ndi 25?

“Dziwani Kuti Ine Ndili Pamodzi ndi Inu Masiku Onse”

Fanizo la Yesu la tirigu ndi namsongole limafotokoza za nthawi yofesa mbewu, kukula ndiponso kukolola. Kodi tsopano tikukhulupirira zotani pa nkhani ya nthawi yokolola?

Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera mwa Anthu Ochepa

Kodi Yesu ankapereka bwanji chakudya chauzimu ku mipingo ya Akhristu oyambirira? Kodi amatsatira njira yomweyo masiku ano?

“Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?”

Nkhaniyi ikusintha zimene tinkakhulupirira ponena za kapolo wokhulupirika ndi wanzeru. Ikusonyeza kuti sitingakhale pa ubwenzi ndi Mulungu popanda kapoloyu.

M’bale Watsopano M’Bungwe Lolamulira

M’bale Mark Sanderson anayamba kutumikira m’Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova pa September 1, 2012.

MBIRI YA MOYO WANGA

Timasangalala Kutumikira Yehova Kwina Kulikonse

Werengani kuti mudziwe zimene banja lina la ku Netherlands lachita kuti lizikhulupirira Yehova ndi mtima wonse ngakhale kuti utumiki wawo unkasinthasintha komanso ankakumana ndi mavuto.

Timasangalala Kutumikira Yehova Kwina Kulikonse

Werengani kuti mudziwe zimene banja lina la ku Netherlands lachita kuti lizikhulupirira Yehova ndi mtima wonse ngakhale kuti utumiki wawo unkasinthasintha komanso ankakumana ndi mavuto.