Mmene Mulungu Amaonera Banja YAMBANI Mmene Mulungu Amaonera Banja Phunzirani mmene Yehova amaonera banja kuchokera m’Baibulo. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Nkhani Zina Mavidiyo Othandiza Kumvetsa Mfundo Zofunika za M’baibulo Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi GALAMUKANI! Mungatani Kuti Musamakangane Pokambirana Mavuto Anu? Amuna ndi akazi amafotokoza maganizo awo mosiyana. Kudziwa mfundoyi kungakuthandizeni kuti musamakangane. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Banja? Mfundo za m’Baibulo zingathandize mwamuna ndi mkazi wake kuti apewe kapenanso kuthetsa mavuto am’banja lawo. KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO Kodi Baibulo Limaloleza Kuthetsa Ukwati? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Mulungu amaloleza komanso zimene amadana nazo. ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA Kuti Mukhale Ndi Banja Losangalala: Muzisonyezana Chikondi Kugwira ntchito, kupanikizika maganizo komanso zochitika za tsiku ndi tsiku zingachititse anthu okwatirana kuti azilephera kusonyezana chikondi. Kodi ndi zotheka kubwezeretsa chikondi m’banja mwanu? ZOKHUDZA IFEYO Fikani Pamsonkhano Dziwani zambiri zokhudza misonkhano yathu. Pezani malo apafupi amene kumachitikira misonkhano yathu. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mmene Mulungu Amaonera Banja Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo Mmene Mulungu Amaonera Banja Chichewa Mmene Mulungu Amaonera Banja https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102020430/univ/art/1102020430_univ_sqr_xl.jpg ebtv