Moyo Wanga Wachinyamata—Ndingatani Ngati Anzanga Amandivutitsa? YAMBANI Moyo Wanga Wachinyamata—Ndingatani Ngati Anzanga Amandivutitsa? Ferin ndi Charlie anaphunzira pa zinthu zovuta zimene anakumana nazo. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Nkhani Zina Zimene Achinyamata Anzanu Amanena Sukulu Mtendere wa M’maganizo Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndingatani Anthu Ena Akamandivutitsa? Anthu ambiri amene akuvutitsidwa amaona kuti palibe chimene angachite. Nkhaniyi ikufotokoza zimene mungachite kuti anthu asiye kukuvutitsani. MAVIDIYO AMAKATUNI Kodi Mungatani Kuti Anzanu Asiye Kukuvutitsani? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu amavutitsa anzawo komanso zimene mungachite kuti asiye kukuvutitsani. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Ndingatani Ngati Anthu Ena Amandivutitsa pa Intaneti? Zimene muyenera kuchita komanso zimene mungachite kuti mudziteteze. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupemphera? Kodi pemphero limangothandiza kuti maganizo akhale m’malo, kapena limathandizanso m’njira zina? ZIMENE ACHINYAMATA ANZANU AMANENA Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhulana Bwino ndi Makolo Anga? Pali zabwino zambiri zimene mungapeze chifukwa cholankhulana bwino ndi makolo anu. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Moyo Wanga Wachinyamata—Ndingatani Ngati Anzanga Amandivutitsa? ZIMENE ACHINYAMATA ANZANU AMANENA Ndingatani Ngati Anzanga Amandivutitsa? Chichewa Ndingatani Ngati Anzanga Amandivutitsa? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502700104/univ/art/502700104_univ_sqr_xl.jpg mtl