Mbiri za a Mboni za Yehova Ena
Padziko lonse, amuna ndi akazi akhala akuika kulambira Yehova pamalo oyamba pamoyo wawo. Nkhani zawo zingakulimbikitseni komanso kulimbitsa chikhulupiriro chanu.
Mbiri za a Mboni za Yehova Ena Zofalitsidwa M’magazini Athu
Pezani malinki a nkhani zosiyanasiyana zofotokoza mbiri za a Mboni za Yehova ena zomwe zinafalitsidwa mu Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! kuyambira mu 1955.
ASTER PARKER
Ndinkafuna Kutumikira Yehova kwa Moyo Wanga Wonse
Aster ankakonda choonadi kuyambira ali mwana. Panthawi imene ku Ethiopia kunali nkhondo chifukwa cha zifukwa za ndale, chikhulupiriro chake chinayesedwa chifukwa chomangidwa. Kenako anakatumikira ku Beteli ya ku New York ndipo anadzakhala ndi ana atatu.
JAY CAMPBELL
Anandichotsa Pafumbi N’kundikweza Pamwamba
Jay wakhala wolumala moyo wake wonse komanso banja lawo linali losauka ndipo sanapite kusukulu. Ngakhale kuti anakumana ndi mavuto onsewa, anaphunzitsa anthu atatu mpaka kufika pobatizidwa ndipo akupitirizabe kuchita utumiki wake mwakhama.
TAPANI VIITALA
Kukwaniritsa Cholinga Changa Chofuna Kuthandiza Anthu Avuto Losamva
Tapani anayendayenda m’mayiko a ku Finland, Estonia, Latvia ndi Lithuania, akulalikira uthenga wabwino kwa anzake avuto losamva. Ngakhale kuti padutsa zaka zoposa 60 kuchokera pomwe anabatizidwa, iye akuchitabe khama kuthandiza anthu avuto losamva
JESÚS MARTÍN
“Yehova Anandipulumutsa M’mavuto Aakulu Kwambiri”
Zaka zimene anali yekhayekha m’chipinda cha ndende chozizira ndiponso chamdima kudzafika nthawi imene anagwira ntchito yosangalatsa ya utumiki wanthawi zonse, Jesús anaphunzira pa zimene zinamuchitikira kudalira mphamvu za Yehova.
DORINA CAPARELLI
Ngakhale Kuti Ndine Wamanyazi, Ndikanasankhanso Kutumikira Yehova
Dorina anatumikirapo ngati mpainiya wokhazikika komanso wapadera. Anatumikiraponso mu utumiki woyang’anira dera ndi chigawo komanso pa Beteli. Munkhaniyi, akufotokoza zomwe anachita pa zaka pafupifupi 70 zomwe ankachita utumiki wanthawi zonse komanso mmene Yehova anamuthandizira ndi kumudalitsa.
MILTIADIS STAVROU
“Taona Yehova Akutisamalira Komanso Kutitsogolera”
Mavuto ndi zinthu zina zosayembekezereka zomwe Milto ndi mkazi wake Doris anakumana nazo akuchita utumiki waumishonale ku Middle East, zinawathandiza kuti azidalira kwambiri Yehova Mulungu m’malo modzidalira.

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha.