Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Amatidziwa Bwino

Amatidziwa Bwino

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Tisanaone kuwala kwa dziko

    Ndipo tisanabadwenso nkomwe,

    Yehova ‘naona kale.

    Anatisonyeza chidwi,

    Amatidziwa bwino.

    (KOLASI)

    Amamva, ‘maona

    Zamumtima mwathumu.

    Tikachita mbali yathu,

    Kayatu tikumva bwanji,

    Amamva, ‘maona,

    Zofuna, zopempha.

    Kaya tisowe chonena amadziwa

    Zonse.

  2. 2. Yehova ndi bambo wachikondi

    Amatikondatu tonsefe.

    Amaona zabwino mwa ife,

    Posachedwapa ‘tidalitsa.

    Amatiganizira.

    (KOLASI)

    Amamva, ‘maona

    Zamumtima mwathumu.

    Tikachita mbali yathu,

    Kayatu tikumva bwanji,

    Amamva, ‘maona,

    Zofuna, zopempha.

    Kaya tisowe chonena amadziwa.

    Zonse.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Ndiye timudalire adzatisonyeza chikondi chake, chake.

    TIzimutulira nkhawa zomwe tili nazo.

    Tisachite mantha amatimvetsa bwino.

    (KOLASI)

    Amamva, ‘maona

    Zamumtima mwathumu.

    Tikachita mbali yathu,

    Kayatu tikumva bwanji,

    Amamva, ‘maona,

    Zofuna, zopempha.

    Kaya tisowe chonena amadziwa.

    (KOLASI)

    Amamva, ‘maona

    Zamumtima mwathumu.

    Tikachita mbali yathu,

    Kayatu tikumva bwanji,

    Amamva, ‘maona

    Zofuna, zopempha.

    Kaya tisowe chonena amadziwa.

    Zonse.