Ndadzipereka Kwa Inu
Pangani Dawunilodi:
1. Usiku kuli bata,
Nyenyezi zikuwala,
Ndikaganiza za ntchito zanu,
Ndimakukondani.
2. Ndikadziperekatu,
Mudzanditsogolera.
Masiku akamadutsa ndithu
Ndidzakhulupirika.
(KOLASI)
Chikhulupiriro
Chathandiza
Kuti ndipirire,
Mwapereka dipo
Mwana wanu,
Ndadziperekadi;
Ndadziperekadi.
3. Mmene dzuwa lawala,
Ndamvatu kutenthera,
M’matidalitsa tsiku ndi tsiku
Ndimayamikiradi.
(KOLASI)
Chikhulupiriro
Chathandiza
Kuti ndipirire,
Mwapereka dipo
Mwana wanu,
Ndadziperekadi;
Ndadziperekadi.
(KOLASI)
Chikhulupiriro
Chathandiza
Kuti ndipirire,
Mwapereka dipo
Mwana wanu,
Ndadziperekadi;
Ndadziperekadi.