Mfundo Zachidule—Chile
- 19,961,000—Chiwerengero cha anthu
- 87,175—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 964—Mipingo
- Pa anthu 232 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
A Mboni Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Madzi Osefukira ku Chile
Madzi atangosefukira ku Chile a Mboni anayamba kuthandiza anthu.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anabala Zipatso Chifukwa Chokonzekera Bwino
Werengani kuti mudziwe mmene mtsikana wina wazaka 10 ku Chile anagwirira ntchito mwakhama kuti aitanire aliyense ku sukulu kwake amene amalankhula chinenero cha Chimapudunguni ku mwambo wofunika kwambiri.