Mboni za Yehova Padziko Lonse

Georgia

  • Gurgeniani, ku Georgia​—Akugawira kabuku kakuti Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?

Mfundo Zachidule—Georgia

  • 3,736,000—Chiwerengero cha anthu
  • 18,841—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 224—Mipingo
  • Pa anthu 199 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Msonkhano Wapadera Woyamba Kuchitika Mumzinda wa Tbilisi ku Georgia

Msonkhano wapaderawu womwe unali woyamba kuchitika ku Georgia, unali wosangalatsa chifukwa panali chakudya chambiri chauzimu, kuchereza alendo, komanso chionetsero cha chikhalidwe ndi mbiri ya dzikolo.

NKHANI

Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Europe Lathandiza Kuti a Mboni za Yehova Akhale ndi Ufulu Wopembedza ku Georgia

Chigamulo chaposachedwapa cha Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Europe chikuteteza ufulu wa a Mboni wosonkhana pamodzi n’cholinga cholambira Mulungu komanso kuuza ena zimene amakhulupirira mwamtendere.

NSANJA YA OLONDA

Chuma Chomwe Chinabisika kwa Zaka Zambiri

Werengani kuti mudziwe zimene zinachitika kuti akatswiri apeze Baibulo lakale kwambiri la Chijojiya.