Mboni za Yehova Padziko Lonse

Guatemala

Mfundo Zachidule—Guatemala

  • 18,918,000—Chiwerengero cha anthu
  • 39,022—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 825—Mipingo
  • Pa anthu 488 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anaona Chikondi cha Abale ndi Alongo

NKHANI

A Mboni za Yehova ndi Okonzeka Kuyamba Ntchito Yomanganso Nyumba Zoonongeka ndi Chivomezi ku Guatemala ndi ku Mexico

A Mboni za Yehova ayamba ntchito yayikulu yothandiza a Mboni anzawo a ku Mexico ndi ku Guatemala amene anakhudzidwa ndi zivomezi ziwiri zomwe zinaononga kwambiri.