Mfundo Zachidule—Marshall Islands
- 61,000—Chiwerengero cha anthu
- 138—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 4—Mipingo
- Pa anthu 496 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Micronesia
Anthu ochokera kumayiko ena amene akutumikira kuzilumba za m’nyanja ya Pacific zimenezi nthawi zambiri amakumana ndi mavuto atatu. Kodi amathana nawo bwanji?