NKHANI
Anamangidwa Chifukwa Chotsatira Zimene Amakhulupirira ku Russia
Oimira gulu lina la zachitetezo la FSB anamanga a Dennis Christensen chifukwa chotenga nawo mbali pa msonkhano wa Mboni za Yehova womwe unkachitika mwamtendere mumzinda wa Oryol ku Russia.
Asilikari a Dziko la Russia Alowa M’dziko la Ukraine—Kodi Zimenezi Zikukwaniritsa Ulosi wa M’Baibulo?
Ngati ndi choncho, kodi Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zithere?
NKHANI
Abale Anathandiza M’bale Konstantin Bazhenov Ali M’ndende, Atatulutsidwa Komanso Pomwe Ankatumizidwa Kwawo
M’bale Konstantin Bazhenov ndi mmodzi mwa a Mboni za Yehova omwe anamalizitsa zaka zake zokhala m’ndende kuchokera pamene Khoti Lalikulu Kwambiri linaletsa ntchito yathu mu 2017. Atakhala m’ndende kwa chaka ndi miyezi 6, anatulutsidwa mofulumirirako pa 5 May 2021. Pambuyo pake anatumizidwa kwawo.
NKHANI
A Mboni za Yehova a ku Irkutsk Anakhalabe Okhulupirika Ngakhale Apolisi Anawachitira Nkhanza
Pa 4 October 2021, apolisi anakafufuza zinthu m’nyumba zingapo m’chigawo cha Irkutsk. Anapanikiza anthu ndi mafunso komanso kuwamenya mwankhanza kwambiri. Pamapeto pake a Mboni za Yehova okwana 6, anakawatsekera m’ndende chifukwa chotsatira zomwe amakhulupirira.