Zoti Muchite Pophunzira Baibulo
Munthu Wakhate Anachiritsidwa
Werengani nkhani ya m’Baibulo yonena za mmene kamtsikana ka ku Isiraeli kanathandizira mkulu wa asilikali a nkhondo wa ku Siriya kuti achiritsidwe. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.