Mariya—Anali Wodzichepetsa ndi Wololera
Mariya anasonyeza kuti ndi wokhulupirika kwa Yehova kwa moyo wake wonse. Kodi mukudziwa munthu wina wofanana naye masiku ano?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
Khalani Bwenzi la Yehova (nyimbo zina)
Mariya—Anali Wodzichepetsa ndi Wololera
Kodi Yehova anagwiritsa ntchito bwanji mtumiki wokhulupirika Mariya? Mvetserani nyimbo yosangalatsa imeneyi ndipo mutsanzira makhalidwe abwino omwe Mariya anali nawo.
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.