Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha
Kodi ndi njira yaikulu kwambiri iti imene Yehova anatisonyeza chikondi?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha (Nyimbo 20)
Nyimbo imene imathandiza mabanja kuti aziyamikira chikondi chimene Yehova ndi Yesu anasonyeza popereka dipo.
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.