Muzigwiritsa Ntchito Nthawi Mwanzeru
Thandizani Kalebe kuzindikira zinthu zofunika kwambiri.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Muzigwiritsa Ntchito Nthawi Mwanzeru
Nthawi ndi mphatso yochokera kwa Yehova. Muziigwiritsa ntchito mwanzeru.
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.