Timakonda Kulambira kwa Pabanja
Kulambira kwa pabanja ndi mphatso yochokera kwa Yehova. Kodi tingamusonyeze bwanji kuti timayamikira mphatsoyi?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
Khalani Bwenzi la Yehova (nyimbo zina)
Timakonda Kulambira kwa Pabanja
Kulambira kwa Pabanja kudzakuthandizani kuti muyandikire kwambiri Yehova.
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.