Kuphunzira za Mabwenzi a Yehova
Tikamaphunzira Baibulo patokha, timakhala ngati tikuyenda ndi mabwenzi a Yehova.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.