Zikomo Kuti Ndinu Mnzanga
Tikhoza kukhala ndi anzathu a misinkhu yosiyanasiyana. Kodi ndi ndani yemwe mukufuna kuti adzakhale mnzanu m’dziko latsopano?
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
Khalani Bwenzi la Yehova (nyimbo zina)
Zikomo Kuti Ndinu Mnzanga
Muzikonda anthu ena ndipo azikhala anzanu apamtima!
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.