February 15-21
NUMERI 3-4
Nyimbo 99 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Utumiki wa Alevi”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)
Num. 4:15—Kodi njila imodzi imene timaonetsela kuti timaopa Mulungu ni iti? (w06 8/1 23 ¶13)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Num. 4:34-49 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 2)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 15)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5.) fg phunzilo 12 ¶8 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Lipoti la Caka ca Utumiki: (Mph. 15.) Nkhani yokambidwa na mkulu. Pambuyo poŵelenga cilengezo cocokela ku ofesi ya nthambi cokhudza lipoti la caka ca utumiki, funsani mafunso ofalitsa amene munawakonzekeletsa pasadakhale kuti asimbe zokumana nazo zolimbikitsa za mu ulaliki m’caka capita ca utumiki.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 22
Mawu Othela (Mph. 3.)
Nyimbo 149 na Pemphelo